Miyambo 31:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chikoka chikhoza kukhala chachinyengo+ ndipo kukongola kukhoza kukhala kopanda phindu,+ koma mkazi woopa Yehova ndi amene amatamandidwa chifukwa cha zochita zake.+ 1 Petulo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.
30 Chikoka chikhoza kukhala chachinyengo+ ndipo kukongola kukhoza kukhala kopanda phindu,+ koma mkazi woopa Yehova ndi amene amatamandidwa chifukwa cha zochita zake.+
4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.