Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 24:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Ndiyeno iwo anayamba kudalitsa Rabeka kuti: “Iwe mlongo wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbewu yako ikalande mizinda ya adani awo.”+

  • Oweruza 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Anthu okhala m’midzi anachoka m’midzi yawo, anachoka m’midzi ya Isiraeli,+

      Kufikira pamene ine Debora+ ndinauka,

      Kufikira pamene ine ndinauka monga mayi mu Isiraeli.+

  • Aroma 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+

  • 1 Petulo 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena