Machitidwe 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira. Machitidwe 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Chotero Baranaba anafunitsitsa kutenga Yohane, wotchedwa Maliko.+
5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira.