Akolose 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Arisitako+ mkaidi mnzanga akuti moni nonse. Komanso Maliko+ msuweni* wa Baranaba, (amene ndinakulangizani kuti mumulandire+ nthawi iliyonse akadzafika kwa inu,) 2 Timoteyo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Luka yekha ndiye amene ali ndi ine. Pobwera utengenso Maliko, pakuti iye ndi wofunika kwa ine chifukwa amandithandiza+ pa utumiki wanga.
10 Arisitako+ mkaidi mnzanga akuti moni nonse. Komanso Maliko+ msuweni* wa Baranaba, (amene ndinakulangizani kuti mumulandire+ nthawi iliyonse akadzafika kwa inu,)
11 Luka yekha ndiye amene ali ndi ine. Pobwera utengenso Maliko, pakuti iye ndi wofunika kwa ine chifukwa amandithandiza+ pa utumiki wanga.