Machitidwe 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma pakati pawo panali amuna ena a ku Kupuro ndi ku Kurene. Amenewa atafika ku Antiokeya anayamba kulankhula ndi anthu olankhula Chigiriki,+ ndipo anali kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa Ambuye Yesu.+
20 Koma pakati pawo panali amuna ena a ku Kupuro ndi ku Kurene. Amenewa atafika ku Antiokeya anayamba kulankhula ndi anthu olankhula Chigiriki,+ ndipo anali kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa Ambuye Yesu.+