Machitidwe 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho ngati Demetiriyo+ ndi amisiri ali nawowa akuimba mlandu munthu, pamakhala masiku a milandu+ ndipo abwanamkubwa+ alipo. Akasumirane kumeneko.
38 Choncho ngati Demetiriyo+ ndi amisiri ali nawowa akuimba mlandu munthu, pamakhala masiku a milandu+ ndipo abwanamkubwa+ alipo. Akasumirane kumeneko.