Yohane 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma adzachita zimenezi chifukwa sanadziwe Atate kapena ine.+ Machitidwe 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo tsopano abale, ndikudziwa kuti munachita zinthu mosadziwa,+ ngati mmenenso olamulira+ anu anachitira.
17 Ndipo tsopano abale, ndikudziwa kuti munachita zinthu mosadziwa,+ ngati mmenenso olamulira+ anu anachitira.