Machitidwe 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko ndi kuona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, anakondwera+ ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize kukhala okhulupirika kwa Ambuye motsimikiza mtima.+ Tito 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Mulungu waonetsa+ kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene kumabweretsa chipulumutso+ kwa anthu, kaya akhale a mtundu wotani.+
23 Atafika kumeneko ndi kuona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, anakondwera+ ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize kukhala okhulupirika kwa Ambuye motsimikiza mtima.+
11 Pakuti Mulungu waonetsa+ kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene kumabweretsa chipulumutso+ kwa anthu, kaya akhale a mtundu wotani.+