Agalatiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti onse odalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wosapitiriza kuyenda m’zinthu zonse zolembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi kuzichita.”+
10 Pakuti onse odalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wosapitiriza kuyenda m’zinthu zonse zolembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi kuzichita.”+