Deuteronomo 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a m’chilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Yeremiya 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukanene kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Munthu aliyense wosamvera mawu a m’pangano limeneli ndi wotembereredwa.+ Machitidwe 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga tsopano n’chifukwa chiyani inu mukumuyesa Mulungu mwa kukanikizira goli pakhosi la ophunzira, goli+ limene makolo athu ngakhalenso ife sitinathe kulisenza?+ Yakobo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aliyense wosunga Chilamulo akalakwitsa mbali imodzi, walakwira malamulo onse.+
26 “‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a m’chilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
3 Ukanene kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Munthu aliyense wosamvera mawu a m’pangano limeneli ndi wotembereredwa.+
10 Nanga tsopano n’chifukwa chiyani inu mukumuyesa Mulungu mwa kukanikizira goli pakhosi la ophunzira, goli+ limene makolo athu ngakhalenso ife sitinathe kulisenza?+