Amosi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga adzatenge zinthu zotsala za Edomu+ ndi mitundu yonse ya anthu imene inali kuitanira pa dzina langa,’+ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.
12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga adzatenge zinthu zotsala za Edomu+ ndi mitundu yonse ya anthu imene inali kuitanira pa dzina langa,’+ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.