2 Akorinto 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuwonjezera pa zinthu za kunja kwa thupi zimenezo, palinso chimene chimandivutitsa maganizo tsiku ndi tsiku, ndicho nkhawa imene ndimakhala nayo pa mipingo yonse.+
28 Kuwonjezera pa zinthu za kunja kwa thupi zimenezo, palinso chimene chimandivutitsa maganizo tsiku ndi tsiku, ndicho nkhawa imene ndimakhala nayo pa mipingo yonse.+