2 Akorinto 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikusautsika ndi kuzunzika kwambiri mumtima, pamodzi ndi misozi yambiri,+ osati kuti muchite chisoni,+ koma kuti mudziwe chikondi chimene ndili nacho makamaka pa inu. Akolose 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna kuti mudziwe nkhondo+ yaikulu imene ndikumenya chifukwa cha inuyo ndi anthu a ku Laodikaya,+ ndi onse amene sanandionepo maso ndi maso.
4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikusautsika ndi kuzunzika kwambiri mumtima, pamodzi ndi misozi yambiri,+ osati kuti muchite chisoni,+ koma kuti mudziwe chikondi chimene ndili nacho makamaka pa inu.
2 Ndikufuna kuti mudziwe nkhondo+ yaikulu imene ndikumenya chifukwa cha inuyo ndi anthu a ku Laodikaya,+ ndi onse amene sanandionepo maso ndi maso.