2 Akorinto 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ngakhale kuti ndinakuchititsani kumva chisoni ndi kalata yanga,+ sindikudandaula. (Ndikuona kuti kalatayo inakuchititsani kumva chisoni, koma kwa kanthawi kochepa.) Chotero, ngakhale kuti poyambapo ndinadandaula,
8 Choncho ngakhale kuti ndinakuchititsani kumva chisoni ndi kalata yanga,+ sindikudandaula. (Ndikuona kuti kalatayo inakuchititsani kumva chisoni, koma kwa kanthawi kochepa.) Chotero, ngakhale kuti poyambapo ndinadandaula,