2 Akorinto 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikusautsika ndi kuzunzika kwambiri mumtima, pamodzi ndi misozi yambiri,+ osati kuti muchite chisoni,+ koma kuti mudziwe chikondi chimene ndili nacho makamaka pa inu. 2 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ena amati: “Makalata ake ndi olemerera ndi amphamvu, koma iyeyo akakhala pakati pathu amaoneka wofooka+ ndipo nkhani zake n’zosagwira mtima.”+
4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikusautsika ndi kuzunzika kwambiri mumtima, pamodzi ndi misozi yambiri,+ osati kuti muchite chisoni,+ koma kuti mudziwe chikondi chimene ndili nacho makamaka pa inu.
10 Pakuti ena amati: “Makalata ake ndi olemerera ndi amphamvu, koma iyeyo akakhala pakati pathu amaoneka wofooka+ ndipo nkhani zake n’zosagwira mtima.”+