2 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ineyo Paulo, ndikukudandaulirani mwa kufatsa+ ndi kukoma mtima+ kwa Khristu, ngakhale kuti ndimaoneka wosanunkha kanthu+ ndikakhala pakati panu, koma wolimba mtima polankhula nanu ndili kwina.+ Agalatiya 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mukudziwa kuti nthawi yoyamba imene ndinalengeza uthenga wabwino kwa inu chifukwa chakuti ndinali kudwala,+
10 Tsopano ineyo Paulo, ndikukudandaulirani mwa kufatsa+ ndi kukoma mtima+ kwa Khristu, ngakhale kuti ndimaoneka wosanunkha kanthu+ ndikakhala pakati panu, koma wolimba mtima polankhula nanu ndili kwina.+
13 Koma mukudziwa kuti nthawi yoyamba imene ndinalengeza uthenga wabwino kwa inu chifukwa chakuti ndinali kudwala,+