2 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ineyo Paulo, ndikukudandaulirani motsanzira Khristu amene ndi wofatsa ndiponso wokoma mtima,+ ngakhale kuti ndimaoneka wofooka ndikakhala pakati panu,+ koma wolimba mtima ndikamalankhula nanu ndili kwina.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Nsanja ya Olonda,4/1/2003, tsa. 248/1/1994, ptsa. 15-16
10 Tsopano ineyo Paulo, ndikukudandaulirani motsanzira Khristu amene ndi wofatsa ndiponso wokoma mtima,+ ngakhale kuti ndimaoneka wofooka ndikakhala pakati panu,+ koma wolimba mtima ndikamalankhula nanu ndili kwina.+