Machitidwe 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pochoka kumeneko anayenda ulendo wa pamadzi wobwerera ku Antiokeya.+ Kumeneku n’kumene m’mbuyomo abale anawaika m’manja mwa Mulungu kuti awasonyeze kukoma mtima kwakukulu n’cholinga choti agwire ntchito imene tsopano anali ataikwaniritsa.+ Aefeso 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinakhala mtumiki+ wa zimenezi mogwirizana ndi mphatso yaulere ya kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene ndinapatsidwa mogwirizana ndi mmene mphamvu yake imagwirira ntchito.+
26 Pochoka kumeneko anayenda ulendo wa pamadzi wobwerera ku Antiokeya.+ Kumeneku n’kumene m’mbuyomo abale anawaika m’manja mwa Mulungu kuti awasonyeze kukoma mtima kwakukulu n’cholinga choti agwire ntchito imene tsopano anali ataikwaniritsa.+
7 Ndinakhala mtumiki+ wa zimenezi mogwirizana ndi mphatso yaulere ya kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene ndinapatsidwa mogwirizana ndi mmene mphamvu yake imagwirira ntchito.+