Machitidwe 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri+ ndi aphunzitsi. Iwo anali Baranaba, Sumeoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo+ wa ku Kurene, Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo, ndi Saulo.
13 Tsopano mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri+ ndi aphunzitsi. Iwo anali Baranaba, Sumeoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo+ wa ku Kurene, Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo, ndi Saulo.