1 Akorinto 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Motero kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda,+ kuti ndipindule Ayuda. Kwa anthu otsatira chilamulo+ ndinakhala ngati wotsatira chilamulo+ kuti ndipindule anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sindili pansi pa chilamulo.
20 Motero kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda,+ kuti ndipindule Ayuda. Kwa anthu otsatira chilamulo+ ndinakhala ngati wotsatira chilamulo+ kuti ndipindule anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sindili pansi pa chilamulo.