-
Machitidwe 5:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Iwo anati: “Ife tapeza ndende ili yokhoma ndi yotetezedwa bwino, alonda ali chilili m’makomo. Koma titatsegula sitinapezemo aliyense.”
-