Luka 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma zinthu zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani nʼkukuzunzani+ ndipo adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakupititsani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:12 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 30
12 Koma zinthu zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani nʼkukuzunzani+ ndipo adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakupititsani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+