Machitidwe 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero kwa nthawi yaitali, anakhala akulankhula molimba mtima chifukwa cha mphamvu ya Yehova. Iye anatsimikizira mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu, mwa kulola kuti zizindikiro ndi zodabwitsa zichitike kudzera mwa ophunzirawo.+
3 Chotero kwa nthawi yaitali, anakhala akulankhula molimba mtima chifukwa cha mphamvu ya Yehova. Iye anatsimikizira mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu, mwa kulola kuti zizindikiro ndi zodabwitsa zichitike kudzera mwa ophunzirawo.+