Mateyu 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero muzichita ndi kutsatira zilizonse zimene angakuuzeni,+ koma musamachite zimene iwo amachita,+ chifukwa iwo amangonena koma osachita.
3 Chotero muzichita ndi kutsatira zilizonse zimene angakuuzeni,+ koma musamachite zimene iwo amachita,+ chifukwa iwo amangonena koma osachita.