Mateyu 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho muzichita ndi kutsatira zinthu zonse zimene angakuuzeni, koma musamachite zimene iwo amachita, chifukwa iwo amangonena koma sachita zimene amanenazo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:3 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, ptsa. 26-27
3 Choncho muzichita ndi kutsatira zinthu zonse zimene angakuuzeni, koma musamachite zimene iwo amachita, chifukwa iwo amangonena koma sachita zimene amanenazo.+