1 Akorinto 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali mwamuna amene anaitanidwa ali wodulidwa?+ Akhalebe wodulidwa. Alipo kodi amene anaitanidwa ali wosadulidwa?+ Asadulidwe.+
18 Kodi pali mwamuna amene anaitanidwa ali wodulidwa?+ Akhalebe wodulidwa. Alipo kodi amene anaitanidwa ali wosadulidwa?+ Asadulidwe.+