Machitidwe 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya+ anapita kumeneko ndi kuyamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa+ malinga ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.” Machitidwe 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tamva kuti ena ochokera pakati pathu akhala akulankhula mawu okusautsani,+ pofuna kupotoza maganizo anu, ngakhale kuti ife sitinawapatse malangizo aliwonse.+
15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya+ anapita kumeneko ndi kuyamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa+ malinga ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.”
24 Tamva kuti ena ochokera pakati pathu akhala akulankhula mawu okusautsani,+ pofuna kupotoza maganizo anu, ngakhale kuti ife sitinawapatse malangizo aliwonse.+