Yesaya 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yang’anani kwa tate+ wanu Abulahamu,+ ndi kwa Sara+ amene anakuberekani ndi zowawa za pobereka. Abulahamuyo anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+ koma ndinamudalitsa ndi kumusandutsa anthu ambiri.+ Yohane 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Poyankha iwo anati: “Atate wathu ndi Abulahamu.”+ Yesu anawauza kuti: “Ngati ndinu ana a Abulahamu,+ chitani ntchito za Abulahamu.
2 Yang’anani kwa tate+ wanu Abulahamu,+ ndi kwa Sara+ amene anakuberekani ndi zowawa za pobereka. Abulahamuyo anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+ koma ndinamudalitsa ndi kumusandutsa anthu ambiri.+
39 Poyankha iwo anati: “Atate wathu ndi Abulahamu.”+ Yesu anawauza kuti: “Ngati ndinu ana a Abulahamu,+ chitani ntchito za Abulahamu.