Aroma 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma tsopano popeza kulibenso gawo limene sindinafikeko m’madera amenewa, ndiponso popeza kuti kwa zaka zambiri ndakhala ndikulakalaka kufika kwanuko,+
23 Koma tsopano popeza kulibenso gawo limene sindinafikeko m’madera amenewa, ndiponso popeza kuti kwa zaka zambiri ndakhala ndikulakalaka kufika kwanuko,+