Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ 1 Akorinto 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komabe tikaweruzidwa,+ ndiye kuti taphunzitsidwa ndi Yehova+ kuti tisalandire chilango+ pamodzi ndi dziko.+
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
32 Komabe tikaweruzidwa,+ ndiye kuti taphunzitsidwa ndi Yehova+ kuti tisalandire chilango+ pamodzi ndi dziko.+