1 Akorinto 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ngati sangathe kudziletsa,+ akwatire, pakuti ndi bwino kukwatira+ kusiyana ndi kuvutika ndi chilakolako.+ 1 Timoteyo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ndimafuna kuti akazi amasiye achitsikana azikwatiwa,+ azibereka ana,+ ndi kusamalira banja, kuti wotsutsa asapeze chifukwa chonenera zachipongwe.+
9 Koma ngati sangathe kudziletsa,+ akwatire, pakuti ndi bwino kukwatira+ kusiyana ndi kuvutika ndi chilakolako.+
14 Choncho ndimafuna kuti akazi amasiye achitsikana azikwatiwa,+ azibereka ana,+ ndi kusamalira banja, kuti wotsutsa asapeze chifukwa chonenera zachipongwe.+