Aroma 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+ Agalatiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwa chilamulo, ine ndinafa ku chilamulo,+ moti sindingachitsatirenso, kuti ndikhale wamoyo kwa Mulungu.+ Akolose 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+
14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+
19 Mwa chilamulo, ine ndinafa ku chilamulo,+ moti sindingachitsatirenso, kuti ndikhale wamoyo kwa Mulungu.+
14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+