Levitiko 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga, zimene ngati munthu azitsatira adzakhaladi ndi moyo chifukwa cha mfundo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.+ Ezekieli 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘“Kumeneko ndinawapatsa malamulo+ ndi kuwadziwitsa zigamulo zanga,+ kuti munthu amene akuzitsatira akhalebe ndi moyo.+ Luka 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo anamuuza kuti: “Wayankha molondola. ‘Uzichita zimenezo, ndipo udzapeza moyo.’”+
5 Muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga, zimene ngati munthu azitsatira adzakhaladi ndi moyo chifukwa cha mfundo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.+
11 “‘“Kumeneko ndinawapatsa malamulo+ ndi kuwadziwitsa zigamulo zanga,+ kuti munthu amene akuzitsatira akhalebe ndi moyo.+