Mateyu 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Opusa ndi akhungu inu! Chofunika kwambiri n’chiti, golide kapena kachisi amene wayeretsa golideyo?+ 2 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamene akuwalonjeza ufulu,+ eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Pakuti aliyense amene wagonjetsedwa, amakhala kapolo kwa womugonjetsayo.+
17 Opusa ndi akhungu inu! Chofunika kwambiri n’chiti, golide kapena kachisi amene wayeretsa golideyo?+
19 Pamene akuwalonjeza ufulu,+ eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Pakuti aliyense amene wagonjetsedwa, amakhala kapolo kwa womugonjetsayo.+