Genesis 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi chilichonse chimene Sara wakhala akunena kwa iwe chokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mvera mawu ake, chifukwa amene adzatchedwa mbewu yako adzachokera mwa Isaki.+ Aheberi 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+
12 Koma Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi chilichonse chimene Sara wakhala akunena kwa iwe chokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mvera mawu ake, chifukwa amene adzatchedwa mbewu yako adzachokera mwa Isaki.+
18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+