Deuteronomo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yehova sanakupatseni mtima woti muthe kuzindikira, maso oti muthe kuona ndi makutu oti muthe kumva, kufikira lero.+ Yeremiya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Tsopano tamverani izi anthu opusa inu, anthu opanda nzeru mumtima mwanu,+ amene muli ndi maso koma simukuona,+ muli ndi makutu koma simukumva.+
4 Koma Yehova sanakupatseni mtima woti muthe kuzindikira, maso oti muthe kuona ndi makutu oti muthe kumva, kufikira lero.+
21 “Tsopano tamverani izi anthu opusa inu, anthu opanda nzeru mumtima mwanu,+ amene muli ndi maso koma simukuona,+ muli ndi makutu koma simukumva.+