Afilipi 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti zondichitikira zija, zathandiza kupititsa patsogolo uthenga wabwino+ m’malo moulepheretsa. 2 Timoteyo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iwe ukhalebe woganiza bwino+ pa zinthu zonse, imva zowawa,+ gwira ntchito ya mlaliki,*+ ndipo ukwaniritse mbali zonse za utumiki wako.+
12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti zondichitikira zija, zathandiza kupititsa patsogolo uthenga wabwino+ m’malo moulepheretsa.
5 Koma iwe ukhalebe woganiza bwino+ pa zinthu zonse, imva zowawa,+ gwira ntchito ya mlaliki,*+ ndipo ukwaniritse mbali zonse za utumiki wako.+