Afilipi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Abale ambiri mwa Ambuye, alimba mtima chifukwa cha kumangidwa kwanga, ndipo akuonetsa kulimba mtima kowonjezereka polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha.+
14 Abale ambiri mwa Ambuye, alimba mtima chifukwa cha kumangidwa kwanga, ndipo akuonetsa kulimba mtima kowonjezereka polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha.+