Yohane 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+
6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+