1 Akorinto 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero anthu azitha kuona kuti ndife atumiki+ a Khristu ndi oyang’anira+ zinsinsi zopatulika+ za Mulungu. Aefeso 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mibadwo ina, chinsinsi+ chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene chaululidwira+ tsopano kwa atumwi ndi aneneri+ ake oyera mwa mzimu.
4 Chotero anthu azitha kuona kuti ndife atumiki+ a Khristu ndi oyang’anira+ zinsinsi zopatulika+ za Mulungu.
5 M’mibadwo ina, chinsinsi+ chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene chaululidwira+ tsopano kwa atumwi ndi aneneri+ ake oyera mwa mzimu.