Agalatiya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Chilamulo chonse chimakwaniritsidwa+ m’mawu akuti: “Uzikonda mnzako ngati mmene umadzikondera wekha.”+ Yakobo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu.
14 Pakuti Chilamulo chonse chimakwaniritsidwa+ m’mawu akuti: “Uzikonda mnzako ngati mmene umadzikondera wekha.”+
8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu.