1 Akorinto 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inunso chimodzimodzi, popeza mukufunitsitsa mphatso za mzimu.+ Chotero, yesetsani kukhala nazo zochuluka kuti mumange mpingo.+ Aheberi 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo tiyeni tiganizirane kuti tilimbikitsane+ pa chikondi ndi ntchito zabwino.+
12 Inunso chimodzimodzi, popeza mukufunitsitsa mphatso za mzimu.+ Chotero, yesetsani kukhala nazo zochuluka kuti mumange mpingo.+