Aroma 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza ndikulakalaka kukuonani+ kuti ndikugawireni mphatso+ inayake yauzimu kuti mukhale olimba,