Aroma 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero, sizidalira munthu wofunayo kapena amene akuthamanga, koma Mulungu,+ amene ali ndi chifundo.+ 2 Akorinto 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene tikugwira naye ntchito limodzi,+ tikukudandauliraninso kuti musalandire kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kuphonya cholinga cha kukoma mtimako.+
16 Chotero, sizidalira munthu wofunayo kapena amene akuthamanga, koma Mulungu,+ amene ali ndi chifundo.+
6 Pamene tikugwira naye ntchito limodzi,+ tikukudandauliraninso kuti musalandire kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kuphonya cholinga cha kukoma mtimako.+