Aroma 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kapena kodi ukunyoza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ kwake ndi kuleza mtima kwake,+ chifukwa chakuti sudziwa kuti cholinga cha kukoma mtima kwa Mulungu ndicho kukuthandiza kuti ulape?+ Aheberi 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+
4 Kapena kodi ukunyoza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ kwake ndi kuleza mtima kwake,+ chifukwa chakuti sudziwa kuti cholinga cha kukoma mtima kwa Mulungu ndicho kukuthandiza kuti ulape?+
15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+