Yohane 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndikupempha m’malo mwa iwo, sindikupemphera dziko,+ koma awo amene mwandipatsa, chifukwa iwo ndi anu. 2 Akorinto 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mukuona zinthu mogwirizana ndi maonekedwe ake akunja.+ Ngati aliyense amakhulupirira mumtima mwake kuti ndi wotsatira Khristu, adziwenso kuti, monga mmene iye alili wotsatira Khristu, ifenso ndife otsatira Khristu.+
9 Choncho ndikupempha m’malo mwa iwo, sindikupemphera dziko,+ koma awo amene mwandipatsa, chifukwa iwo ndi anu.
7 Mukuona zinthu mogwirizana ndi maonekedwe ake akunja.+ Ngati aliyense amakhulupirira mumtima mwake kuti ndi wotsatira Khristu, adziwenso kuti, monga mmene iye alili wotsatira Khristu, ifenso ndife otsatira Khristu.+