Aroma 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndani adzatilekanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Chisautso kodi, kapena zowawa, chizunzo, njala, usiwa, zoopsa, kapena lupanga?+
35 Ndani adzatilekanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Chisautso kodi, kapena zowawa, chizunzo, njala, usiwa, zoopsa, kapena lupanga?+