1 Akorinto 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero pasakhale munthu wodzitama chifukwa cha anthu, popeza zinthu zonse ndi zanu,+ Yakobo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma tsopano mumakonda kudzitama.+ Kunyada konse koteroko ndi koipa.