Agalatiya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa mtanda wonse.+ 2 Timoteyo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndipo mawu awo adzafalikira ngati chilonda chonyeka.+ Ena mwa anthu amenewo ndi Hemenayo ndi Fileto.+
17 ndipo mawu awo adzafalikira ngati chilonda chonyeka.+ Ena mwa anthu amenewo ndi Hemenayo ndi Fileto.+