Yohane 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho ngati Mwana wakumasulani, mudzakhaladi omasuka.+ Filimoni 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sukhala nayenso monga kapolo,+ koma woposa kapolo.+ Ukhala naye monga m’bale amene ine ndimamukonda kwambiri,+ ndipo iwe uyenera kumukonda koposa pamenepo popeza iye ndi kapolo wako ndi m’bale wako mwa Ambuye.
16 Sukhala nayenso monga kapolo,+ koma woposa kapolo.+ Ukhala naye monga m’bale amene ine ndimamukonda kwambiri,+ ndipo iwe uyenera kumukonda koposa pamenepo popeza iye ndi kapolo wako ndi m’bale wako mwa Ambuye.